Genesis 42:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mukabweretse m’bale wanu wamng’onoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukadzatero, ndidzakubwezerani m’bale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda m’dziko lino.’”+ Luka 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Atabwerera kwawo pambuyo polandira ufumuwo, analamula kuti akapolo ake aja amene anawapatsa ndalama zasiliva abwere kwa iye, kuti awerengerane ndi kuona mmene apindulira pa malonda awo.+
34 Mukabweretse m’bale wanu wamng’onoyo kwa ine kuti ndidzatsimikize kuti si inu akazitape koma anthu achilungamo. Mukadzatero, ndidzakubwezerani m’bale wanuyu, ndipo mudzatha kuchita malonda m’dziko lino.’”+
15 “Atabwerera kwawo pambuyo polandira ufumuwo, analamula kuti akapolo ake aja amene anawapatsa ndalama zasiliva abwere kwa iye, kuti awerengerane ndi kuona mmene apindulira pa malonda awo.+