Genesis 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukhale nafe kwathu kuno, dziko lino likhalanso lanu. Mukhazikike, ndipo muzichita malonda mwaufulu.”+ Genesis 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno mukabweretse mng’ono wanuyo kwa ine. Mukatero, ndidzatsimikiza kuti mukunena zoona, ndipo simudzaphedwa.”+ Iwo anavomereza kuchita zimenezo. Yakobo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tamverani tsopano inu amene mumati: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko ndi kupeza phindu.”+
10 Mukhale nafe kwathu kuno, dziko lino likhalanso lanu. Mukhazikike, ndipo muzichita malonda mwaufulu.”+
20 Ndiyeno mukabweretse mng’ono wanuyo kwa ine. Mukatero, ndidzatsimikiza kuti mukunena zoona, ndipo simudzaphedwa.”+ Iwo anavomereza kuchita zimenezo.
13 Tamverani tsopano inu amene mumati: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko ndi kupeza phindu.”+