Yakobo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tamverani inu amene mumanena kuti: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko nʼkupeza phindu.”+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:13 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 21
13 Tamverani inu amene mumanena kuti: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko nʼkupeza phindu.”+