Yakobo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tamverani tsopano inu amene mumati: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko ndi kupeza phindu.”+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:13 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 21
13 Tamverani tsopano inu amene mumati: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko ndi kupeza phindu.”+