Miyambo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usadzitame ndi zamawa+ chifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.+ Luka 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anati, ‘Ndichita izi:+ Ndipasula nkhokwe zanga ndi kumanga zikuluzikulu, ndipo tirigu wanga yense ndi zinthu zanga zonse zabwino ndidzazitutira mmenemo.+
18 Ndiyeno anati, ‘Ndichita izi:+ Ndipasula nkhokwe zanga ndi kumanga zikuluzikulu, ndipo tirigu wanga yense ndi zinthu zanga zonse zabwino ndidzazitutira mmenemo.+