Luka 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anati, ‘Ndichita izi:+ Ndigwetsa nyumba zanga zosungiramo zinthu nʼkumanga zikuluzikulu, ndipo tirigu wanga yense ndi zinthu zanga zonse ndidzazitutira mmenemo, Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:18 Nsanja ya Olonda,11/15/1998, tsa. 19
18 Ndiyeno anati, ‘Ndichita izi:+ Ndigwetsa nyumba zanga zosungiramo zinthu nʼkumanga zikuluzikulu, ndipo tirigu wanga yense ndi zinthu zanga zonse ndidzazitutira mmenemo,