Genesis 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Simiyoni ndi Levi m’pachibale pawo.+ Malupanga awo ndiwo zida zochitira zachiwawa.+