Genesis 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+ Genesis 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamutcha Levi.*+ Genesis 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.
33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+
34 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamutcha Levi.*+
23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.