Genesis 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pa tsiku lachitatu, pamene anthuwo anali pa ululu,+ ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi,+ alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake n’kukalowa mumzindawo mosaonetsera cholinga chawo. Kenako anayamba kupha mwamuna aliyense.+ Genesis 42:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yosefe anapita payekha kukalira.+ Kenako anabwerako n’kuyambiranso kulankhula nawo, ndipo anatenga Simiyoni+ n’kumumanga iwo akuona.+ Genesis 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Simiyoni ndi Levi m’pachibale pawo.+ Malupanga awo ndiwo zida zochitira zachiwawa.+ 1 Mbiri 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana a Simiyoni anali Nemueli,+ Yamini,+ Yaribi, Zera, ndi Shauli.+ Chivumbulutso 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mu fuko la Simiyoni,+ 12,000.Mu fuko la Levi,+ 12,000.Mu fuko la Isakara,+ 12,000.
25 Koma pa tsiku lachitatu, pamene anthuwo anali pa ululu,+ ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi,+ alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake n’kukalowa mumzindawo mosaonetsera cholinga chawo. Kenako anayamba kupha mwamuna aliyense.+
24 Ndiyeno Yosefe anapita payekha kukalira.+ Kenako anabwerako n’kuyambiranso kulankhula nawo, ndipo anatenga Simiyoni+ n’kumumanga iwo akuona.+