Genesis 43:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano Yosefe anachokapo mofulumira chifukwa anagwidwa chifundo mumtima poona m’bale wakeyo.+ Anafunafuna malo oti akalirire, ndipo analowa m’chipinda chamkati n’kukagwetsa misozi.+
30 Tsopano Yosefe anachokapo mofulumira chifukwa anagwidwa chifundo mumtima poona m’bale wakeyo.+ Anafunafuna malo oti akalirire, ndipo analowa m’chipinda chamkati n’kukagwetsa misozi.+