Genesis 43:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo mwamunayo anati: “Musachite mantha,+ simunalakwe kanthu. Mulungu wanu, Mulungu wa bambo anu ndiye anakupatsani chumacho m’matumba mwanu.+ Ndalama zanu zinafikira kwa ine.” Atatero mwamunayo anamasula Simiyoni n’kumubweretsa kwa iwo.+ Yobu 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu akamangidwa m’matangadza,+Amagwidwa ndi zingwe za masautso.
23 Pamenepo mwamunayo anati: “Musachite mantha,+ simunalakwe kanthu. Mulungu wanu, Mulungu wa bambo anu ndiye anakupatsani chumacho m’matumba mwanu.+ Ndalama zanu zinafikira kwa ine.” Atatero mwamunayo anamasula Simiyoni n’kumubweretsa kwa iwo.+