Genesis 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini,+ Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wachikanani. Ekisodo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wachikanani.+ Amenewa ndiwo mabanja a fuko la Simiyoni.+
10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini,+ Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wachikanani.
15 Ndipo ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wachikanani.+ Amenewa ndiwo mabanja a fuko la Simiyoni.+