Numeri 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amenewa ndiwo anali mabanja a Asimiyoni. Amuna onse pamodzi analipo 22,200.+ Yoswa 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana a Isiraeli anapereka mizinda, kuchokera m’fuko la ana a Yuda ndi fuko la ana a Simiyoni. Mizindayo anachita kuitchula mayina.+
9 Ana a Isiraeli anapereka mizinda, kuchokera m’fuko la ana a Yuda ndi fuko la ana a Simiyoni. Mizindayo anachita kuitchula mayina.+