1 Mbiri 6:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Komanso, atachita maere anawapatsa mizinda imeneyi kuchokera ku fuko la ana a Yuda,+ fuko la ana a Simiyoni,+ ndi fuko la ana a Benjamini.+ Mizindayo anachita kuitchula mayina.
65 Komanso, atachita maere anawapatsa mizinda imeneyi kuchokera ku fuko la ana a Yuda,+ fuko la ana a Simiyoni,+ ndi fuko la ana a Benjamini.+ Mizindayo anachita kuitchula mayina.