1 Mbiri 6:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ana a Aroni anawapatsa mzinda* wothawirako+ wa Heburoni,+ mzinda wa Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Yatiri,+ mzinda wa Esitemowa+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mbiri 6:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 mzinda wa Hileni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Debiri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
57 Ana a Aroni anawapatsa mzinda* wothawirako+ wa Heburoni,+ mzinda wa Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Yatiri,+ mzinda wa Esitemowa+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
58 mzinda wa Hileni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Debiri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,