1 Mbiri 6:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Mbadwa za Aroni anazipatsa mzinda wothawirako+ wa Heburoni,+ mzinda wa Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Yatiri,+ mzinda wa Esitemowa ndi malo ake odyetserako ziweto,+
57 Mbadwa za Aroni anazipatsa mzinda wothawirako+ wa Heburoni,+ mzinda wa Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Yatiri,+ mzinda wa Esitemowa ndi malo ake odyetserako ziweto,+