Yoswa 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya mʼdera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ mʼdera lamapiri la Efuraimu komanso Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, mʼdera lamapiri la Yuda. Yoswa 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imeneyi inali mizinda imene inasankhidwa kuti Aisiraeli onse ndi alendo okhala pakati pawo, azithawirako akapha munthu mwangozi,+ kuti asaphedwe ndi wobwezera magazi asanakaonekere pamaso pa oweruza.*+
7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya mʼdera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ mʼdera lamapiri la Efuraimu komanso Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, mʼdera lamapiri la Yuda.
9 Imeneyi inali mizinda imene inasankhidwa kuti Aisiraeli onse ndi alendo okhala pakati pawo, azithawirako akapha munthu mwangozi,+ kuti asaphedwe ndi wobwezera magazi asanakaonekere pamaso pa oweruza.*+