Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 33:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Atachoka ku Padani-aramu,+ Yakobo anafika bwino kumzinda wa Sekemu,+ mʼdziko la Kanani.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo.

  • Yoswa 21:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mabanja a ana a Kohati, kapena kuti Alevi otsala, anapatsidwa mizinda yochokera mʼfuko la Efuraimu pambuyo pochita maere. 21 Anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake,+ wa Sekemu,+ ndi malo ake odyetserako ziweto mʼdera lamapiri la Efuraimu. Anawapatsanso Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena