Genesis 42:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati mulidi achilungamo, mmodzi wa inu atsale m’ndendemu.+ Ena nonsenu pitani, mukapereke tirigu kunyumba zanu chifukwa kuli njala.+ Genesis 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Simiyoni ndi Levi m’pachibale pawo.+ Malupanga awo ndiwo zida zochitira zachiwawa.+
19 Ngati mulidi achilungamo, mmodzi wa inu atsale m’ndendemu.+ Ena nonsenu pitani, mukapereke tirigu kunyumba zanu chifukwa kuli njala.+