Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pagulu lawo, moyo wanga usakhale nawo.+ Maganizo anga asagwirizane ndi mpingo wawo,+ chifukwa atakwiya anapha anthu,+ ndipo mwankhanza zawo, anapundula* ng’ombe zamphongo.

  • Genesis 49:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Utembereredwe mkwiyo wawo+ chifukwa ndi wankhanza,+ ndi ukali wawo chifukwa umachita mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+

  • Salimo 140:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Anthu amene amakonza chiwembu mumtima mwawo,+

      Amene amandiukira tsiku lonse ngati mmene zimakhalira pankhondo.+

  • Mika 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena