Yoswa 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere+ achiwiri anagwera Simiyoni, kapena kuti fuko la ana a Simiyoni,+ potsata mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.+ Yoswa 21:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mizinda yonse ya Alevi m’dziko limene ana a Isiraeli anapatsidwa inalipo 48,+ pamodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+
19 Maere+ achiwiri anagwera Simiyoni, kapena kuti fuko la ana a Simiyoni,+ potsata mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.+
41 Mizinda yonse ya Alevi m’dziko limene ana a Isiraeli anapatsidwa inalipo 48,+ pamodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+