Genesis 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+
6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+