Genesis 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Yosefe,*+ ndipo anati: “Yehova wandiwonjezera mwana wina wamwamuna.” 1 Samueli 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mkaziyu atatsala pang’ono kumwalira, amayi amene anaima pambali pake anayamba kulankhula kuti: “Usachite mantha, pakuti wabereka mwana wamwamuna.”+ Koma iye sanayankhe kapena kuikirapo mtima.
24 Chotero Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Yosefe,*+ ndipo anati: “Yehova wandiwonjezera mwana wina wamwamuna.”
20 Mkaziyu atatsala pang’ono kumwalira, amayi amene anaima pambali pake anayamba kulankhula kuti: “Usachite mantha, pakuti wabereka mwana wamwamuna.”+ Koma iye sanayankhe kapena kuikirapo mtima.