Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ana amene Rakele anaberekera Yakobo anali Yosefe ndi Benjamini.

  • Genesis 45:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo Yosefe anauza abale akewo kuti: “Senderani pafupi ndi ine.” Ndipo anasenderadi pafupi naye.

      Ndiyeno Yosefe anati: “Ndine m’bale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+

  • Deuteronomo 33:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo kwa Yosefe anati:+

      “Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+

      Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+

      Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+

  • Machitidwe 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+

  • Chivumbulutso 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mu fuko la Zebuloni,+ 12,000.

      Mu fuko la Yosefe,+ 12,000.

      Ndipo mu fuko la Benjamini,+ anadindamo anthu 12,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena