Genesis 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yosefe anauza abale akewo kuti: “Sunthirani pafupi ndi ine.” Ndipo anasunthiradi pafupi ndi iye. Kenako Yosefe anati: “Ndine mʼbale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+
4 Ndiyeno Yosefe anauza abale akewo kuti: “Sunthirani pafupi ndi ine.” Ndipo anasunthiradi pafupi ndi iye. Kenako Yosefe anati: “Ndine mʼbale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+