Genesis 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamene amalonda a Chimidiyani+ aja ankadutsa, abale a Yosefe anamutulutsa mʼchitsimemo nʼkumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo amalondawo anapita naye ku Iguputo. Machitidwe 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitu ya mabanjayo inachitira nsanje Yosefe+ nʼkumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+
28 Pamene amalonda a Chimidiyani+ aja ankadutsa, abale a Yosefe anamutulutsa mʼchitsimemo nʼkumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo amalondawo anapita naye ku Iguputo.