Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+