1 Mbiri 1:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano awa ndiwo mafumu amene analamulira dziko la Edomu+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+ Bela mwana wa Beori. Dzina la mzinda wake linali Dinihaba.+
43 Tsopano awa ndiwo mafumu amene analamulira dziko la Edomu+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+ Bela mwana wa Beori. Dzina la mzinda wake linali Dinihaba.+