Genesis 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Rakele atabereka Yosefe, nthawi yomweyo Yakobo anauza Labani kuti: “Ndiloleni ndizipita kwathu, kudziko lakwathu.+ Genesis 46:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Rakele,+ mkazi wa Yakobo, anali Yosefe+ ndi Benjamini.+
25 Rakele atabereka Yosefe, nthawi yomweyo Yakobo anauza Labani kuti: “Ndiloleni ndizipita kwathu, kudziko lakwathu.+