Genesis 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndili nawe ndipo ndikuyang’anira pa ulendo wako wonse, kufikira ndidzakubwezera kumalo ano.+ Sindidzakusiya kufikira nditachitadi zimene ndanena kwa iwe.”+ Genesis 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ uja, kumene unadzoza mwala+ kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+
15 Ine ndili nawe ndipo ndikuyang’anira pa ulendo wako wonse, kufikira ndidzakubwezera kumalo ano.+ Sindidzakusiya kufikira nditachitadi zimene ndanena kwa iwe.”+
13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ uja, kumene unadzoza mwala+ kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+