Genesis 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Farao anafunsa abale ake a Yosefe aja kuti: “Kodi mumagwira ntchito yanji?”+ Iwo anayankha Farao kuti: “Akapolo anufe timaweta nkhosa+ monga ankachitira makolo athu.”+
3 Ndiyeno Farao anafunsa abale ake a Yosefe aja kuti: “Kodi mumagwira ntchito yanji?”+ Iwo anayankha Farao kuti: “Akapolo anufe timaweta nkhosa+ monga ankachitira makolo athu.”+