Genesis 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ng’ombe ndi abulu. Anamupatsanso antchito aamuna ndi aakazi, komanso abulu aakazi ndi ngamila.+ Genesis 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anakhala ndi nkhosa ndi ng’ombe zankhaninkhani. Anakhalanso ndi antchito ochuluka kwambiri,+ moti Afilisitiwo anayamba kum’chitira kaduka.+ Genesis 46:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+
16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ng’ombe ndi abulu. Anamupatsanso antchito aamuna ndi aakazi, komanso abulu aakazi ndi ngamila.+
14 Iye anakhala ndi nkhosa ndi ng’ombe zankhaninkhani. Anakhalanso ndi antchito ochuluka kwambiri,+ moti Afilisitiwo anayamba kum’chitira kaduka.+
34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+