Genesis 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zitatero, Abulahamu anaika Sara mkazi wake m’manda kuphanga la Makipela, moyang’anizana ndi Mamure, kapena kuti Heburoni, m’dziko la Kanani.+ Genesis 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Potsirizira pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ m’dera la Kiriyati-ariba,+ komwe ndi ku Heburoni. Uku n’kumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+
19 Zitatero, Abulahamu anaika Sara mkazi wake m’manda kuphanga la Makipela, moyang’anizana ndi Mamure, kapena kuti Heburoni, m’dziko la Kanani.+
27 Potsirizira pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ m’dera la Kiriyati-ariba,+ komwe ndi ku Heburoni. Uku n’kumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+