Genesis 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Isiraeli anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa ana ake ena onse,+ chifukwa anali mwana amene anam’bereka atakalamba. Chotero anam’soketsera mkanjo wamizeremizere wamanja aatali.+ 1 Timoteyo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+
3 Isiraeli anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa ana ake ena onse,+ chifukwa anali mwana amene anam’bereka atakalamba. Chotero anam’soketsera mkanjo wamizeremizere wamanja aatali.+
24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+