Luka 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokhulupirika pa chinthu chaching’ono alinso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu wosalungama pa chinthu chaching’ono alinso wosalungama pa chinthu chachikulu.+ Luka 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuuza kuti, ‘Unagwira ntchito, ndiwe kapolo wabwino! Chifukwa wasonyeza kukhulupirika pa chinthu chaching’ono, ndakupatsa ulamuliro woyang’anira mizinda 10.’+
10 Munthu wokhulupirika pa chinthu chaching’ono alinso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu wosalungama pa chinthu chaching’ono alinso wosalungama pa chinthu chachikulu.+
17 Iye anamuuza kuti, ‘Unagwira ntchito, ndiwe kapolo wabwino! Chifukwa wasonyeza kukhulupirika pa chinthu chaching’ono, ndakupatsa ulamuliro woyang’anira mizinda 10.’+