Miyambo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wanga, ochimwa akayesa kukunyengerera usavomere.+ Miyambo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero pali chifukwa chanji choti usangalalire ndi mkazi wachilendo mwana wanga, kapena choti ukumbatirire chifuwa cha mkazi wina?+ Miyambo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Phunzitsa mwana m’njira yomuyenerera.+ Ngakhale akadzakalamba sadzapatukamo.+
20 Chotero pali chifukwa chanji choti usangalalire ndi mkazi wachilendo mwana wanga, kapena choti ukumbatirire chifuwa cha mkazi wina?+