Luka 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso ngati simunakhale wokhulupirika pa zinthu za ena,+ ndani adzakupatseni mphoto imene anakusungirani? 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
12 Komanso ngati simunakhale wokhulupirika pa zinthu za ena,+ ndani adzakupatseni mphoto imene anakusungirani?