Miyambo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti milomo ya mkazi wachilendo imakha uchi ngati chisa cha njuchi+ ndipo m’kamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+ Miyambo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakamwa pa akazi achilendo pali ngati dzenje lakuya.+ Wotsutsidwa ndi Yehova adzagweramo.+
3 Pakuti milomo ya mkazi wachilendo imakha uchi ngati chisa cha njuchi+ ndipo m’kamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+