Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+

  • Danieli 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komabe mkulu wa nduna za panyumba ya mfumuyo anauza Danieli kuti: “Ine ndikuopa mbuye wanga mfumu, amene walamula kuti mupatsidwe zakudya ndi zakumwa zake.+ Ndiye n’chifukwa chiyani mukufuna kuti aone nkhope zanu zili zachisoni poyerekeza ndi ana ena amsinkhu wanu? Komanso, bwanji mukufuna kuikitsa mutu wanga pangozi kwa mfumu?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena