Genesis 41:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinaonanso ngala zina 7 zikutuluka pambuyo pa zoyamba zija. Zimenezi zinali zonyala ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa.+
23 Ndinaonanso ngala zina 7 zikutuluka pambuyo pa zoyamba zija. Zimenezi zinali zonyala ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa.+