Genesis 41:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anaonanso ngala zina 7 zikutuluka pambuyo pa zoyambazo.+ Ngalazo zinali zonyala ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa.+ Salimo 129:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati udzu wanthete womera padenga,+Umene umauma asanauzule,+
6 Anaonanso ngala zina 7 zikutuluka pambuyo pa zoyambazo.+ Ngalazo zinali zonyala ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa.+