Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+

      Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+

      Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+

      Ngati udzu womera padenga+ ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+

  • Ezekieli 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ngakhale kuti mtengowo anautenga pamalo ena n’kukaubzala pamalo ena, kodi zinthu zidzauyendera bwino? Kodi sudzaumiratu ukadzawombedwa ndi mphepo ya kum’mawa?+ Udzauma ndithu pamalo amene unabzalidwapo.”’”+

  • Hoseya 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Ndipo iye akayamba kubereka ndi kutulutsa ana ngati bango,+ mphepo ya kum’mawa, mphepo ya Yehova idzabwera.+ Mphepo yake ikuchokera kuchipululu ndipo idzaumitsa chitsime chake ndi kuphwetsa kasupe wake.+ Ameneyo adzawononga chuma chimene chikuphatikizapo zinthu zosiririka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena