Yeremiya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu. Hoseya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mphepo yawakulunga m’mapiko ake,+ ndipo iwo adzachita manyazi ndi nsembe zawo.”+
11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu.