Ezekieli 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pamapeto pake, mtengowo unazulidwa ndi manja aukali+ n’kuponyedwa pansi. Kenako kunabwera mphepo ya kum’mawa n’kuumitsa zipatso zake.+ Ndodo yake yolimba inathyoledwa n’kuuma+ ndipo inanyeka ndi moto.+
12 Koma pamapeto pake, mtengowo unazulidwa ndi manja aukali+ n’kuponyedwa pansi. Kenako kunabwera mphepo ya kum’mawa n’kuumitsa zipatso zake.+ Ndodo yake yolimba inathyoledwa n’kuuma+ ndipo inanyeka ndi moto.+