Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Ezekieli 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtengowotu umangoikidwa pamoto basi kuti ukhale nkhuni.+ Motowo umanyeketsa kutsinde ndi kunsonga kwake. Pakati pa mtengowo pamapsanso.+ Choncho kodi mtengowo ungagwire ntchito ina iliyonse?
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
4 Mtengowotu umangoikidwa pamoto basi kuti ukhale nkhuni.+ Motowo umanyeketsa kutsinde ndi kunsonga kwake. Pakati pa mtengowo pamapsanso.+ Choncho kodi mtengowo ungagwire ntchito ina iliyonse?