Salimo 80:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Watenthedwa ndi moto ndi kudulidwa.+Iwo amawonongeka ndi kudzudzula kwa pankhope panu.+ Yohane 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+
6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+