-
Ezekieli 15:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mtengowo umaponyedwa pamoto kuti ukhale nkhuni ndipo motowo umanyeketsa kutsinde ndi kunsonga kwake. Pakati pa mtengowo pamapsanso. Ndiye kodi ungagwire ntchito iliyonse?
-