Ezekieli 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtengowotu umangoikidwa pamoto basi kuti ukhale nkhuni.+ Motowo umanyeketsa kutsinde ndi kunsonga kwake. Pakati pa mtengowo pamapsanso.+ Choncho kodi mtengowo ungagwire ntchito ina iliyonse?
4 Mtengowotu umangoikidwa pamoto basi kuti ukhale nkhuni.+ Motowo umanyeketsa kutsinde ndi kunsonga kwake. Pakati pa mtengowo pamapsanso.+ Choncho kodi mtengowo ungagwire ntchito ina iliyonse?