Yesaya 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu wamphamvu adzakhala ngati chingwe chabwazi,+ ndipo ntchito yake idzakhala ngati kamoto kakang’ono. Zonsezi zidzayakira limodzi popanda wozizimitsa.”+ Amosi 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Ndinabweretsa chiwonongeko pakati pa anthu inu chofanana ndi chimene Mulungu anabweretsa pa Sodomu ndi Gomora.+ Pamenepo inu munakhala ngati chitsa cholanditsidwa pamoto+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.
31 Munthu wamphamvu adzakhala ngati chingwe chabwazi,+ ndipo ntchito yake idzakhala ngati kamoto kakang’ono. Zonsezi zidzayakira limodzi popanda wozizimitsa.”+
11 “‘Ndinabweretsa chiwonongeko pakati pa anthu inu chofanana ndi chimene Mulungu anabweretsa pa Sodomu ndi Gomora.+ Pamenepo inu munakhala ngati chitsa cholanditsidwa pamoto+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.