Genesis 41:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno ngala zonyalazo zinayamba kumeza ngala 7 zooneka bwinozo.+ Malotowo ndinawafotokoza kwa ansembe amatsenga,+ koma palibe ndi mmodzi yemwe amene anatha kundimasulira.”+
24 Ndiyeno ngala zonyalazo zinayamba kumeza ngala 7 zooneka bwinozo.+ Malotowo ndinawafotokoza kwa ansembe amatsenga,+ koma palibe ndi mmodzi yemwe amene anatha kundimasulira.”+